Luka 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:37 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 125/15/1994, ptsa. 26-27 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Anna analankhula zokhudza mwanayo (gnj 1 48:52–50:21)
37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.