Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 3 Nsanja ya Olonda,4/1/2012, tsa. 9
2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+