Luka 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anali kuchita zimenezi monga mmene analembera m’buku la mawu a Yesaya mneneri kuti: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Yesaya 1, ptsa. 399-401
4 Anali kuchita zimenezi monga mmene analembera m’buku la mawu a Yesaya mneneri kuti: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.+