Luka 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzenje lililonse likwiriridwe, ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zisalazidwe. Njira zokhotakhota zikhale zowongoka ndipo malo okumbikakumbika akhale osalala bwino.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Yesaya 1, ptsa. 399-401
5 Dzenje lililonse likwiriridwe, ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zisalazidwe. Njira zokhotakhota zikhale zowongoka ndipo malo okumbikakumbika akhale osalala bwino.+