Luka 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo anayamba kuuza khamu la anthu obwera kwa iye kudzabatizidwa kuti: “Ana a njoka inu,+ ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+
7 Pamenepo anayamba kuuza khamu la anthu obwera kwa iye kudzabatizidwa kuti: “Ana a njoka inu,+ ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+