Luka 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Yesu anawayankha kuti: “Kodi simunawerenge zimene Davide+ anachita pamene iye ndi amuna amene anali naye anamva njala?+
3 Koma Yesu anawayankha kuti: “Kodi simunawerenge zimene Davide+ anachita pamene iye ndi amuna amene anali naye anamva njala?+