Yohane 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sikuti iyeyu anali kuwalako ayi,+ koma anangobwera kudzachitira umboni+ za kuwalako.