Yohane 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anavomereza osakana ayi. Anavomereza ndithu, kuti: “Ine sindine Khristu ayi.”+