Yohane 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Izi zinachitikira ku Betaniya wa kutsidya lina la Yorodano, kumene Yohane anali kubatiza anthu.+