-
Yohane 1:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Pamenepo Yesu anacheuka. Atawaona akumutsatira, anawafunsa kuti: “Kodi mukufunafuna chiyani?” Iwo anati: “Rabi, (dzina lotanthauza, Mphunzitsi, polimasulira,) kodi mukukhala kuti?”
-