Yohane 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo,+ kuti asamaone ndi maso awowo, asazindikire ndi mitima yawo ndi kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:40 Yesu—Ndi Njira, tsa. 242 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 8
40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo,+ kuti asamaone ndi maso awowo, asazindikire ndi mitima yawo ndi kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+