Yohane 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yudasi,+ wina osati Isikariyoti, anati: “Ambuye, bwanji mukufuna kudzionetsera bwinobwino kwa ife koma osati ku dzikoli?”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 275 Nsanja ya Olonda,8/1/1990, tsa. 9
22 Yudasi,+ wina osati Isikariyoti, anati: “Ambuye, bwanji mukufuna kudzionetsera bwinobwino kwa ife koma osati ku dzikoli?”+