Yohane 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano Simoni Petulo ndiponso wophunzira wina anali kutsatira Yesu.+ Wophunzira winayu anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe, chotero analowa pamodzi ndi Yesu m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Buku la Onse, ptsa. 16-17 Nsanja ya Olonda,4/1/1991, tsa. 3111/15/1990, tsa. 8
15 Tsopano Simoni Petulo ndiponso wophunzira wina anali kutsatira Yesu.+ Wophunzira winayu anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe, chotero analowa pamodzi ndi Yesu m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe.
18:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Buku la Onse, ptsa. 16-17 Nsanja ya Olonda,4/1/1991, tsa. 3111/15/1990, tsa. 8