Machitidwe 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Amuna inu, abale anga, ndilankhula ndithu mwaufulu za kholo lathu Davide. Iye anamwalira+ ndi kuikidwa m’manda, ndipo manda ake tili nawo mpaka lero. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:29 Nsanja ya Olonda,9/15/1996, tsa. 9
29 “Amuna inu, abale anga, ndilankhula ndithu mwaufulu za kholo lathu Davide. Iye anamwalira+ ndi kuikidwa m’manda, ndipo manda ake tili nawo mpaka lero.