Machitidwe 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo zimenezi ndinazichitadi mu Yerusalemu. Oyera ambiri ndinawatsekera m’ndende,+ nditapatsidwa mphamvu ndi ansembe aakulu.+ Pamene anafuna kuwapha, ine ndinali kuvomereza. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:10 Nsanja ya Olonda,6/15/1999, tsa. 30
10 Ndipo zimenezi ndinazichitadi mu Yerusalemu. Oyera ambiri ndinawatsekera m’ndende,+ nditapatsidwa mphamvu ndi ansembe aakulu.+ Pamene anafuna kuwapha, ine ndinali kuvomereza.