2 Akorinto 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye.
2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye.