2 Akorinto 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ndipitiriza kuchita zimene ndikuchita,+ kuti nditsekereze anthu amene akuyesayesa kupeza chifukwa choti anamizire kuti ndi ofanana ndi ife, podzitamandira chifukwa cha udindo wawo.
12 Tsopano ndipitiriza kuchita zimene ndikuchita,+ kuti nditsekereze anthu amene akuyesayesa kupeza chifukwa choti anamizire kuti ndi ofanana ndi ife, podzitamandira chifukwa cha udindo wawo.