2 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2021, tsa. 26 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, ptsa. 26-27
23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+