Aefeso 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano, kodi mawu akuti “anakwera kumwamba”+ amatanthauza chiyani? Amatanthauza kuti anayamba watsika pansi, padziko.+
9 Tsopano, kodi mawu akuti “anakwera kumwamba”+ amatanthauza chiyani? Amatanthauza kuti anayamba watsika pansi, padziko.+