Akolose 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zili motero chifukwa kunamukomera Mulungu kuti zinthu zonse+ zikhale mwa mwana wakeyo ndipo zidzazemo bwino. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 24
19 Zili motero chifukwa kunamukomera Mulungu kuti zinthu zonse+ zikhale mwa mwana wakeyo ndipo zidzazemo bwino.