Akolose 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ineyo ndikugwira ntchito mwakhama kuti ndichite zimenezi, poyesetsa kwambiri+ mogwirizana ndi mphamvu+ yake imenenso ikugwira ntchito mwa ine.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:29 Nsanja ya Olonda,12/15/1994, tsa. 13
29 Ineyo ndikugwira ntchito mwakhama kuti ndichite zimenezi, poyesetsa kwambiri+ mogwirizana ndi mphamvu+ yake imenenso ikugwira ntchito mwa ine.+