1 Timoteyo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, anandichitira chifundo+ kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire+ n’cholinga chakuti adzapeze moyo wosatha.+
16 Komabe, anandichitira chifundo+ kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire+ n’cholinga chakuti adzapeze moyo wosatha.+