1 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,10/15/1996, tsa. 17
11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+