1 Timoteyo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati ndingachedwe, ndalemba izi kuti udziwe mmene uyenera kuchitira m’nyumba ya Mulungu,+ imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo. Mpingowo ndi umene umalimbikitsa ndi kuteteza+ choonadi. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Nsanja ya Olonda,4/15/2007, tsa. 29
15 Koma ngati ndingachedwe, ndalemba izi kuti udziwe mmene uyenera kuchitira m’nyumba ya Mulungu,+ imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo. Mpingowo ndi umene umalimbikitsa ndi kuteteza+ choonadi.