2 Timoteyo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, ngati munthu akuchita nawo mpikisano ngakhale pa masewera,+ savekedwa nkhata yaulemerero kumutu akapanda kupikisana nawo motsatira malamulo. 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 81/1/2001, ptsa. 28-29
5 Komanso, ngati munthu akuchita nawo mpikisano ngakhale pa masewera,+ savekedwa nkhata yaulemerero kumutu akapanda kupikisana nawo motsatira malamulo.