2 Timoteyo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kumbukira kuti, malinga ndi uthenga wabwino umene ndikulalikira,+ Yesu Khristu anauka kwa akufa+ ndipo anali mbewu ya Davide.+
8 Kumbukira kuti, malinga ndi uthenga wabwino umene ndikulalikira,+ Yesu Khristu anauka kwa akufa+ ndipo anali mbewu ya Davide.+