Yakobo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Nsanja ya Olonda,11/15/2008, tsa. 2011/15/1997, tsa. 24
20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+