1 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti zili bwino ngati wina, chifukwa cha chikumbumtima chake kwa Mulungu, akupirira zowawa ndi kuvutika popanda mlandu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,11/1/1990, tsa. 27
19 Pakuti zili bwino ngati wina, chifukwa cha chikumbumtima chake kwa Mulungu, akupirira zowawa ndi kuvutika popanda mlandu.+