Chivumbulutso 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:15 Nsanja ya Olonda,7/15/2015, tsa. 16 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112
15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri.