Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Lowani muthanthwe ndipo dzibiseni m’fumbi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake.+

  • Yesaya 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mulungu akadzaimirira kuti dziko lapansi linjenjemere, anthu adzalowa m’mapanga a m’matanthwe ndi m’mayenje a m’nthaka chifukwa cha kuopsa kwa Yehova,+ ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake.+

  • Ezekieli 33:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, ndithu anthu amene ali m’malo owonongedwa adzaphedwa ndi lupanga.+ Munthu amene ali kutchire ndidzam’pereka kwa chilombo cholusa kuti akhale chakudya chake.+ Anthu amene ali m’malo otetezeka ndi m’mapanga+ adzafa ndi mliri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena