Chivumbulutso 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 16 Utumiki Komanso Moyo Wathu,12/2019, tsa. 2 Nsanja ya Olonda,2/15/2010, tsa. 171/15/2010, ptsa. 21, 239/15/2008, tsa. 285/1/2002, ptsa. 30-3111/15/2000, tsa. 147/1/1996, ptsa. 20-212/1/1995, ptsa. 15-16, 18-191/1/1988, tsa. 17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 124, 126
15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze.
7:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 16 Utumiki Komanso Moyo Wathu,12/2019, tsa. 2 Nsanja ya Olonda,2/15/2010, tsa. 171/15/2010, ptsa. 21, 239/15/2008, tsa. 285/1/2002, ptsa. 30-3111/15/2000, tsa. 147/1/1996, ptsa. 20-212/1/1995, ptsa. 15-16, 18-191/1/1988, tsa. 17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 124, 126