10 Ndipo ndinamva mawu ofuula kumwamba, akuti:
“Tsopano chipulumutso,+ mphamvu,+ ufumu wa Mulungu wathu,+ ndi ulamuliro wa Khristu+ wake zafika, chifukwa woneneza abale athu waponyedwa pansi. Iyeyo anali kuwaneneza usana ndi usiku pamaso pa Mulungu wathu.+