Chivumbulutso 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinaona chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake,+ ndi nambala+ ya dzina lake, ndinawaona ataimirira pambali pa nyanja yagalasiyo,+ ali ndi azeze+ a Mulungu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 216-217
2 Kenako ndinaona chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake,+ ndi nambala+ ya dzina lake, ndinawaona ataimirira pambali pa nyanja yagalasiyo,+ ali ndi azeze+ a Mulungu.