Mawu a M'munsi
b Galamukani! sisankha mtundu uliwonse wa chithandizo. Akristu ayenera kuonetsetsa kuti chithandizo chilichonse chimene akulandira sichikutsutsana ndi mfundo za chikhalidwe za Baibulo. Kuti mudziƔe zambiri onani Nsanja ya Olonda ya October 15, 1988, masamba 25-9.