Mawu a M'munsi
a Onani nkhani yakuti “Zaka Zoposa 40 Tili Oletsedwa Kupembedza mu Ulamuliro wa Chikomyunizimu,” mu Nsanja ya Olonda ya March 1, 1999 patsamba 24-9, ndiponso yakuti “Pamene Anatitengera ku Ukapolo ku Siberia!” mu Galamukani! wa May 8, 1999 patsamba 20-5.