Mawu a M'munsi
c Mukhoza kudziwa zimene Baibulo limanena pa nkhani zosiyanasiyana m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Bukuli mukhoza kulipeza mwaulere kwa a Mboni za Yehova kapena mukhoza kuliwerenga pa Webusaiti ya www.jw.org.