Mawu a M'munsi
c Kuti muone chikalata chonse, onani buku la 1974 Yearbook of Jehovah’s Witnesses, masamba 208 mpaka 209. Nkhani ya munthu amene anapulumuka nawo pa ulendo umenewu mungaipeze mu Nsanja ya Olonda ya January 1, 1998, masamba 25 mpaka 29.