Mawu a M'munsi
a Kuti mumve zambiri pankhani yolemberana chikalata cha mapangano a malondayi, onani Nsanja ya Olonda ya August 1, 1997, masamba 30 ndi 31; Nsanja ya Olonda ya November 15, 1986, masamba 16 ndi 17; ndiponso Galamukani! ya Chingelezi ya February 8, 1983, masamba 13 mpaka 15. Magaziniwa ndi ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.