April Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano ya April 2016 Zitsanzo za Ulaliki April 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 16-20 Tizilimbikitsa Anzathu Powayankhula Mokoma Mtima MOYO WATHU WACHIKHRISTU Nkhani Zatsopano Zothandiza Poyamba Kukambirana ndi Anthu April 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 21-27 Yobu Sanalole Kuti Maganizo Olakwika Amusokoneze April 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 28-32 Yobu Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kukhala ndi Mtima Wosagawanika April 25–May 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 33-37 Mnzako Weniweni Amakuuza Malangizo Othandiza KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Ntchito Yoitanira Anthu Kumsonkhano Wachigawo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo