June Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya June 2017 Zitsanzo za Ulaliki June 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 51–52 Nthawi Zonse Mawu a Yehova Amakwaniritsidwa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumakhulupirira Kwambiri Zimene Yehova Analonjeza? June 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIRO 1-5 Mtima Wodikira Umatithandiza Kuti Tipirire June 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 1-5 Ezekieli Anasangalala Kulengeza Uthenga wa Mulungu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzisangalala Mukamalalikira Uthenga Wabwino June 26–July 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 6-10 Kodi Mudzalembedwa Chizindikiro Choti Ndinu Woyenera Kupulumuka? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizitsatira Mfundo za Makhalidwe Abwino za Yehova