October Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 2020 Zimene Tinganene October 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 31-32 Thawani Kulambira Mafano MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muziona Kuti Ubwenzi Wanu Ndi Yehova Ndi Wamtengo Wapatali October 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 33-34 Makhalidwe Abwino Kwambiri a Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Achinyamata, Kodi Yehova Ndi Mnzanu Wapamtima? October 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 35-36 Anathandizidwa Kugwira Ntchito ya Yehova October 26–November 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 37-38 Maguwa Ansembe a Chihema Anali Ofunika pa Kulambira Koona MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tidzagwira Ntchito Yapadera mu November Yolengeza za Ufumu wa Mulungu