September Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 2020 Zimene Tinganene September 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 23-24 Musamatsatire Khamu la Anthu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Musamafalitse Nkhani Zabodza September 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 25-26 Chinthu Chofunika Kwambiri M’chihema September 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 27-28 Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zovala za Ansembe? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kulalikira Tili pa Kamera Kapena Pogwiritsa Ntchito Intakomu September 28–October 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 29-30 Chopereka kwa Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mungapereke Nthawi ndi Mphamvu Zanu?