Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 1
  • Makhalidwe a Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Makhalidwe a Yehova
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Makhalidwe a Yehova
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Mikhalidwe ya Yehova
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kodi ‘Angelo Ankhope 4 Aliyense’ Akuimira Chiyani?
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • “Onetsani Kuwala Kwanu” Kuti Yehova Alemekezeke
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 1

Nyimbo 1

Makhalidwe a Yehova

Losindikizidwa

(Chivumbulutso 4:11)

1. Yehova Mulungu, wamphamvu,

Mwini moyo komanso kuwala.

Mphamvu zanu zimaonekera

M’zinthu zomwe munalenga.

2. Ndinu Mfumu ya chilungamo,

Mumatiphunzitsa malamulo.

Tikamaphunzira Mawu anu,

Timaona nzeru zanu.

3. Chikondi chanu ndi changwiro.

Sitingathe kukubwezerani.

Makhalidwe anu n’ngapamwamba,

Tidzalengeza mokondwa.

(Onaninso Sal. 36:9; 145:​6-13; Yak. 1:17.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena