Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsamba 4
  • Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Fanizo la Matalente?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Fanizo la Matalente
    Nsanja ya Olonda—1989
  • Fanizo la Ndalama
    Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako
  • Fanizo la Ndalama 10 za Mina
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 August tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 19-20

Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina

19:12-24

Mbuye, akapolo komanso matumba a ndalama

Kodi zinthu zosiyanasiyana zotchulidwa m’fanizoli zikuimira chiyani?

  1. Mbuye akuimira Yesu

  2. Akapolo akuimira Akhristu odzozedwa

  3. Ndalama zimene mbuye anapatsa akapolo ake zikuimira mwayi wapadera wothandiza ena kuti akhale ophunzira a Yesu

M’fanizoli, Yesu anachenjeza Akhristu odzozedwa za zimene zingachitike ngati atayamba kukhala ndi mtima wangati wa kapolo woipa. Yesu amayembekezera kuti otsatira ake azigwiritsa ntchito nthawi, mphamvu komanso zinthu zawo pogwira ntchito yophunzitsa anthu.

Kodi ndingatsanzire bwanji Akhristu odzozedwa pogwira ntchito yophunzitsa anthu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena