Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsamba 4
  • August 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 August tsamba 4

August 13-19

Luka 19-20

  • Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina”: (10 min.)

    • Luka 19:12, 13​—“Munthu wina wa m’banja lachifumu” asanachoke, anapatsa akapolo ake ndalama kuti achite bizinesi mpaka adzabwere (jy 232 ¶2-4)

    • Luka 19:16-19​—Akapolo okhulupirika anali ndi luso losiyanasiyana koma aliyense analandira mphoto (jy 232 ¶7)

    • Luka 19:20-24​—Zinthu sizinamuyendere bwino kapolo woipa yemwe sanachite malonda ndi ndalama imene anapatsidwa (jy 233 ¶1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 19:43​—Kodi mawu a Yesuwa anakwaniritsidwa bwanji? (”adzamanga mpanda wazisonga kukuzungulira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 19:43, nwtsty)

    • Luka 20:38​—Kodi zimene Yesu ananenazi zikutitsimikizira bwanji kuti akufa adzaukitsidwa? (“pakuti kwa iye onsewa ndi amoyo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 20:38, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 19:11-27

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w14 8/15 29-30​—Mutu: Kodi Mawu a Yesu a pa Luka 20:34-36, Amanena za Kuukitsidwa kwa Anthu Odzakhala Padziko Lapansi?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 83

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Yesetsani Kudziwa Bwino Webusaiti Yathu ya JW.ORG”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy tsamba 6-7, pamutu wakuti, Njira, Choonadi ndi Moyo

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena