Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 13
  • Titsanzire Yesu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Titsanzire Yesu
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Mzinda Wodabwitsa Wopangidwa Ndi Mapepala
    Galamukani!—2012
  • Kodi Tizitchula Zinthu Ziti Tikamapemphera kwa Mulungu?
    Galamukani!—2012
  • Tizichita Zinthu Mogwirizana ndi Pemphero la Ambuye—Gawo 1
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Yehova Amatipatsa Zimene Timafunikira Tsiku Lililonse
    Nsanja ya Olonda—2004
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 13

NYIMBO 13

Titsanzire Yesu

Losindikizidwa

(1 Petulo 2:​21)

  1. 1. Yehova Mulungu

    Anatikondadi,

    Anapereka Yesu monga dipo.

    Yesu analola

    Kudzakhala munthu.

    Anayeretsa dzina la M’lungu.

  2. 2. Yesu ankakonda

    Mawu a Mulungu.

    Ndi amene ankamupatsa nzeru.

    Ankatumikira

    Mokhulupirika

    Ndipo anasangalatsa M’lungu.

  3. 3. Titsanzire

    Yesu Potamanda M’lungu

    Komanso muzochita zathu zonse.

    Tizimutsanzira

    M’moyo wathu wonse

    Ndipo tizisangalatsa M’lungu.

(Onaninso Yoh. 8:29; Aef. 5:2; Afil. 2:​5-7.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena