Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsamba 4
  • Yakobo ndi Labani Anachita Pangano Lamtendere

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yakobo ndi Labani Anachita Pangano Lamtendere
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Yakobo Anaona Zinthu Zauzimu Kukhala Zofunika
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Yakobo Amka ku Harana
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Pangano Latsopano la Mulungu Liyandikira Kukwaniritsidwa Kwake
    Chisungiko cha Padziko Lonse mu Ulamuliro wa “Kalonga wa Mtendere”
  • ‘Mudzakhala Ufumu wa Ansembe’
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 April tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 31

Yakobo ndi Labani Anachita Pangano Lamtendere

31:44-53

N’chifukwa chiyani Yakobo ndi Labani anaunjika mulu wamiyala?

  • Unali ngati umboni kwa anthu onse kuti anachita pangano la mtendere

  • Unkawakumbutsa kuti Yehova akuona ngati akukwaniritsa pangano lawo

Chithunzi choyamba: Alongo awiri ali ku Nyumba ya Ufumu ndipo akuyang’anana mokwiya. Abale ndi alongo ena akucheza komanso kuseka. Chachiwiri: Alongo awiri aja ali limodzi kumalo odyera ndipo akumwa khofi kwinaku akucheza. Patebulopo pali mphatso komanso Baibulo.

Masiku anonso, Yehova amafuna kuti tizikhala mwamtendere ndi abale komanso alongo athu. Kodi zinthu zitatu zotsatirazi zingatithandize bwanji kuti tizikhala mwamtendere ndi ena?

  • Kukambirana momasuka.​—Mt 5:23, 24

  • Kukhululukirana ndi mtima wonse.​—Akl 3:13

  • Kukhala woleza mtima.​—Aro 12:21

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena