Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 July tsamba 6
  • Kufunika kwa Mwambo wa Pasika kwa Akhristu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kufunika kwa Mwambo wa Pasika kwa Akhristu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Pasika ndi Chiyani?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Mliri wa 10
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • ‘Tsikuli Lidzakhala Chikumbutso Chanu’
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Kuchokera ku Seder Kumka ku Chipulumutso
    Nsanja ya Olonda​—1990
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 July tsamba 6
Banja la Chiisiraeli lisanatuluke mu Iguputo likudya Pasika litaimirira.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 12

Kufunika kwa Mwambo wa Pasika kwa Akhristu

12:5-7, 12, 13, 24-27

Aisiraeli ankayenera kumvera malangizo omwe anapatsidwa ndi Yehova kuti asakhudzidwe ndi mliri wa 10. (Eks 12:28) Usiku wa pa Nisani 14, mabanja anauzidwa kuti akhale m’nyumba zawo. Iwo ankafunika kupha mwanawankhosa wamphongo wa chaka chimodzi kapena mbuzi. Anauzidwanso kuti awaze magazi a nyamayo pamafelemu a m’mbali mwa khomo komanso pafelemu la pamwamba pa chitseko. Kenako ankafunika kuwotcha nyama yonseyo n’kuidya mofulumira. Aliyense sankafunika kutuluka m’nyumba yake mpaka m’mawa.​—Eks 12:9-11, 22.

Kodi kumvera kumatiteteza m’njira ziti masiku ano?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena