Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 108
  • Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Chikondi cha Mulungu N’chosatha
    Imbirani Yehova
  • Chikondi cha Mulungu Chokhulupirika
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kodi Timapindula Bwanji ndi Chikondi Chokhulupirika cha Yehova?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • Kodi Mumasangalala ndi Chikondi Chokhulupirika Ngati Mmene Yehova Amachitira?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 108

NYIMBO 108

Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu

Losindikizidwa

(Yesaya 55:1-3)

  1. 1. M’lungu ndi chikondi.

    Amatikonda kwambiri.

    Anaperekatu Yesu

    Kuwombola anthu onse,

    Ndipo tikudikirira

    Moyo wosangalatsadi.

    (KOLASI)

    Inu nonse a ludzu

    Dzamweni kwaulere

    Madzi opatsa moyo.

    M’lungu ndi chikondi.

  2. 2. M’lungu ndi chikondi.

    Ntchito zake ndi umboni.

    Anasonyeza chikondi

    Popatsa Yesu Ufumu.

    Ufumu wake tsopano

    Wayamba kulamulira.

    (KOLASI)

    Inu nonse a ludzu

    Dzamweni kwaulere

    Madzi opatsa moyo.

    M’lungu ndi chikondi.

  3. 3. M’lungu ndi chikondi.

    Nafenso tichisonyeze.

    Tiphunzitse anthu onse

    Malamulo a Mulungu.

    Timamvera M’lungu wathu

    Polalikira konseko.

    (KOLASI)

    Inu nonse a ludzu

    Dzamweni kwaulere

    Madzi opatsa moyo.

    M’lungu ndi chikondi.

(Onaninso Sal. 33:5; 57:10; Aef. 1:7.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena