Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • nwt tsamba 2228-2229
  • B9 Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Amene Danieli Analosera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • B9 Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Amene Danieli Analosera
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Babulo
  • Mediya ndi Perisiya
  • Girisi
  • Roma
  • Britain ndi America
  • Kuimirira ndi Kugwa kwa Fano lalikulu
    Samalani Ulosi wa Danieli!
  • Ndani Adzalamulira Dziko?
    Samalani Ulosi wa Danieli!
  • Masinthidwe a Dziko Onenedweratu Kufikira ku Ufumu wa Mulungu
    Boma Lathu la Dziko Likudza’lo—Ufumu wa Mulungu
  • Mfundo Zazikulu za M’buku la Danieli
    Nsanja ya Olonda—2007
Onani Zambiri
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
B9 Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Amene Danieli Analosera

B9

Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Amene Danieli Analosera

Losindikizidwa
Chifaniziro kapena fano, la mu Danieli chaputala 2
Mkango wamapiko kuimira ufumu wa Babulo

Babulo

Danieli 2:32, 36-38; 7:4

Mfumu Nebukadinezara anawononga Yerusalemu mu 607 B.C.E.

Chimbalangondo kuimira ufumu wa Mediya ndi Perisiya

Mediya ndi Perisiya

Danieli 2:32, 39; 7:5

Anagonjetsa Babulo mu 539 B.C.E.

Koresi analamula kuti Ayuda abwerere ku Yerusalemu mu 537 B.C.E.

Kambuku wamapiko kuimira ufumu wa Girisi

Girisi

Danieli 2:32, 39; 7:6

Alekizanda Wamkulu anagonjetsa Perisiya mu 331 B.C.E.

Chilombo choopsa cha nyanga 10, kuimira ufumu wa Roma ndi wa Britain ndi America womwe ndi ufumu wamphamvu kwambiri padziko lonse

Roma

Danieli 2:33, 40; 7:7

Anayamba kulamulira Isiraeli mu 63 B.C.E.

Anawononga Yerusalemu mu 70 C.E.

Britain ndi America

Danieli 2:33, 41-43

Mu 1914-1918 C.E. Mayiko a Britain ndi America anayamba kulamulira dziko lonse mkati mwa Nkhondo Yoyamba ya Padziko Lonse

  • Kumene Malo Akupezeka Pamapu

  • Sade

  • Yerusalemu

  • Ekibatana

  • Babulo

  • Ufumu wa Babulo

  • Tema

  • Susa, Susani

  • Pesepoli

  • Ufumu wa Mediya ndi Perisiya

  • Ufumu wa Roma

  • Roma

  • Pela

  • Konsitantinopo (Bezantiyamu)

  • Alekizandiriya

  • Yerusalemu

  • Antiokeya

  • Selukeya

  • Ufumu wa Girisi

  • Zimene zili pamapu

  • Ufumu wa Babulo

  • Ufumu wa Mediya ndi Perisiya

  • Ufumu wa Girisi

  • Ufumu wa Roma

  • Dera lomwe likulamuliridwa ndi maufumu onse awiri

  • Tchati Chosonyeza Nthawi

  • 607 B.C.E. Ufumu wa Babulo unawononga Yerusalemu

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena